2 Samueli 19:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo anthu onse anaoloka Yordani, ndi mfumu yomwe inaoloka; ndipo mfumuyo inapsompsona Barizilai nimdalitsa; ndipo iye anabwerera kunka kumalo kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo anthu onse anaoloka Yordani, ndi mfumu yomwe inaoloka; ndipo mfumuyo inapsompsona Barizilai nimdalitsa; ndipo iye anabwerera kunka kumalo kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Choncho anthu onse adaoloka Yordani, nayonso mfumu idaoloka. Ndipo mfumu idampsompsona Barizilai, nimdalitsa, ndipo iye adabwerera kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Kotero anthu onse anawoloka Yorodani ndipo kenaka mfumu inawoloka. Mfumu inapsompsona Barizilai ndi kumupatsa madalitso ndipo Barizilaiyo anabwerera kwawo. Onani mutuwo |