Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 17:3 - Buku Lopatulika

3 ndipo anthu onsewo ndidzabwera nao kwa inu; munthu mumfunayo ali ngati onse obwerera; momwemo anthu onse adzakhala mumtendere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 ndipo anthu onsewo ndidzabwera nao kwa inu; munthu mumfunayo ali ngati onse obwerera; momwemo anthu onse adzakhala mumtendere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Tsono anthu onse ndidzabwera nawo kwa inu, ngati mkwati amene akubwerera kwa mwamuna wake. Imfa ya munthu mmodzi yekha, idzakhalitsa anthu onse pa mtendere.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 ndipo anthu onse ndidzabwera nawo kwa inu, ngati mkwati amene akubwerera kwa mwamuna wake. Imfa ya munthu mmodzi yekha idzakhalitsa anthu onse pa mtendere.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 17:3
6 Mawu Ofanana  

Ndipo mauwa anamuyenerera Abisalomu, ndi akulu onse a Israele.


Pomwepo Abinere anati kwa Davide, Ndidzanyamuka ndi kupita ndi kusonkhanitsira mfumu mbuye wanga Aisraele onse, kuti adzapangane nanu pangano, ndi kuti mukhale mfumu pa zonse mtima wanu uzikhumba. Chomwecho Davide analawirana ndi Abinere, namuka iye mumtendere.


Kulibe mtendere, ati Yehova, kwa oipa.


Palibe mtendere, ati Mulungu wanga, kwa oipa.


Ndiponso apoletsa bala la anthu anga pang'onong'ono, ndi kuti, Mtendere, mtendere; koma palibe mtendere.


Pamene angonena, Mtendere ndi mosatekeseka, pamenepo chionongeko chobukapo chidzawagwera, monga zowawa mkazi wa pakati; ndipo sadzapulumuka konse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa