2 Samueli 17:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ngakhale ngwazi imene mtima wake ukunga mtima wa mkango idzasungunuka konse, pakuti Aisraele onse adziwa atate wanu kuti ndiye munthu wamphamvu, ndi iwo ali naye ndiwo ngwazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ngakhale ngwazi imene mtima wake ukunga mtima wa mkango idzasungunuka konse, pakuti Aisraele onse adziwa atate wanu kuti ndiye munthu wamphamvu, ndi iwo ali naye ndiwo ngwazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono ngakhale munthu wolimba mtima ngati mkango adzaguluka m'nkhongono. Paja Aisraele onse akudziŵa kuti bambo wanu ndi munthu wamphamvu, ndipo kuti anthu amene ali nawowo ngolimba mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tsono ngakhale msilikali wolimba mtima kwambiri, amene mtima wake uli ngati wa mkango, adzagwidwa ndi mantha aakulu pakuti Aisraeli akudziwa kuti abambo anu ndi ankhondo ndipo kuti iwo amene ali nawo ndi anthu olimba mtima. Onani mutuwo |