2 Samueli 16:18 - Buku Lopatulika18 Husai nanena ndi Abisalomu, Iai; koma amene Yehova anasankha ndi anthu awa, ndi anthu onse a Israele, ine ndili wake, ndipo ndidzakhala naye iyeyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Husai nanena ndi Abisalomu, Iai; koma amene Yehova anasankha ndi anthu awa, ndi anthu onse a Israele, ine ndili wake, ndipo ndidzakhala naye iyeyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Apo Husai adayankha Abisalomu kuti, “Iyai, munthu amene wasankhidwa ndi Chauta ndiponso ndi anthu aŵa, kudzanso amuna onse a Aisraele, ndiye ndidzakhale mtumiki wake, ndipo ndidzakhala pambuyo pake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Husai anati kwa Abisalomu, “Ayi, ndidzakhala wake wa amene Yehova wamusankha, wosankhidwa ndi anthu awa ndi anthu onse a Israeli, ndipo ndidzakhala wake nthawi zonse. Onani mutuwo |