Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 14:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo Abisalomu anakhala ku Yerusalemu zaka ziwiri zathunthu, osaona nkhope ya mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo Abisalomu anakhala ku Yerusalemu zaka ziwiri zathunthu, osaona nkhope ya mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Choncho Abisalomu adakhala zaka ziŵiri zathunthu mu Yerusalemu, osaonekera kwa mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Abisalomu anakhala zaka ziwiri mu Yerusalemu osaonekera kwa mfumu.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 14:28
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Yakobo anati, Iaitu, ngatitu ndapeza ufulu pamaso panu, mulandire mphatso yanga padzanja langa; pakuti popeza ndinaona nkhope yanu, monga anthu aona nkhope ya Mulungu, ndipo inu mwandivomereza ine.


Ndipo Yuda ananena ndi iye kuti, Munthu uja anatilimbitsira mau kuti, simudzaonanso nkhope yanga, koma mphwanu akhale ndi inu ndiko.


Ndipo mfumu inati, Apatukire kunyumba ya iye yekha, koma asaone nkhope yanga. Chomwecho Abisalomu anapatukira kunyumba ya iye yekha, wosaona nkhope ya mfumu.


Pamenepo Abisalomu anaitana Yowabu kuti akamtumize iye kwa mfumu; koma anakana kubwera kwa iye; ndipo anamuitananso nthawi yachiwiri, koma anakana kubwera.


Tsono mfumu Solomoni anatuma anthu nakamtsitsa ku guwa la nsembe. Iye nadza, nagwadira mfumu Solomoni; Solomoni nati kwa iye, Pita kwanu.


Ndipo mfumu inatuma munthu kukaitana Simei, nati kwa iye, Udzimangire nyumba mu Yerusalemu, nukhale komweko osatulukako kunka kwina konse.


Yang'anirani kuti musanyoze mmodzi wa ang'ono awa; pakuti ndinena kwa inu, kuti angelo ao apenya chipenyere nkhope ya Atate wanga wa Kumwamba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa