Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 14:23 - Buku Lopatulika

23 Chomwecho Yowabu ananyamuka nanka ku Gesuri, nabwera naye Abisalomu ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Chomwecho Yowabu ananyamuka namka ku Gesuri, nabwera naye Abisalomu ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Choncho Yowabu adanyamuka, adapita ku Gesuri, nakatenga Abisalomu, nkubwera naye ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Choncho Yowabu anapita ku Gesuri ndipo anamubweretsa Abisalomu ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 14:23
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yowabu anagwa nkhope yake pansi, namlambira, nadalitsa mfumuyo; nati Yowabu, Lero mnyamata wanu ndadziwa kuti munandikomera mtima, mbuye wanga mfumu, popeza mfumu yachita chopempha mnyamata wake.


wachiwiri Kiliyabu, wa Abigaile mkazi wa Nabala wa ku Karimele; ndi wachitatu Abisalomu mwana wa Maaka mwana wamkazi wa Talimai mfumu ya ku Gesuri;


Yairi mwana wa Manase analanda dziko lonse la Arigobu, kufikira malire a Agesuri ndi Amaakati; nalitcha dzina lake, Basani Havoti-Yairi, kufikira lero lino).


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa