2 Samueli 14:14 - Buku Lopatulika14 Pakuti kufa tidzafa, ndipo tili ngati madzi otayika pansi amene sangathe kuwaolanso; ngakhale Mulungu sachotsa moyo, koma alingalira njira yakuti wotayikayo asakhale womtayikira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pakuti kufa tidzafa, ndipo tili ngati madzi otayika pansi amene sakhoza kuwaolanso; ngakhale Mulungu sachotsa moyo, koma alingalira njira yakuti wotayikayo asakhale womtayikira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Paja madzi akatayika saoleka, ndiye tonsefe tiyenera kufa ndithu. Koma Mulungu safuna kuti moyo wa munthu utayike, tsono amakonza njira yakuti wopirikitsidwa asakhale wotayikiratu chonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Koma poti madzi akatayika sawoleka, ndiye tonsefe tiyenera kufa ndithu. Koma Mulungu safuna kuti moyo wa munthu utayike kotero anakonza njira yakuti wopirikitsidwayo asakhale wotayikiratu. Onani mutuwo |