2 Samueli 14:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mfumu inati, Ubwere naye kwa ine aliyense wakunena kanthu ndi iwe, ndipo iyeyo sadzakukhudzanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mfumu inati, Ubwere naye kwa ine aliyense wakunena kanthu ndi iwe, ndipo iyeyo sadzakukhudzanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Apo mfumu idati, “Ngati wina aliyense akunenerani kanthu kena kalikonse, mubwere naye kwa ine, ndipo sadzakuvutitsaninso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mfumu inayankha kuti, “Ngati wina aliyense anene kanthu kwa iwe, umubweretse kwa ine, ndipo sadzakuvutitsanso.” Onani mutuwo |