2 Samueli 11:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo pakufika kwa iye Uriya uja, Davide anamfunsa kuti, Yowabu ali bwanji? Ndi anthu ali bwanji? Ndi nkhondo ili bwanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo pakufika kwa iye Uriya uja, Davide anamfunsa kuti, Yowabu ali bwanji? Ndi anthu ali bwanji? Ndi nkhondo ili bwanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Uriya atabwera, Davide adamufunsa m'mene analiri Yowabu kunkhondoko, ndiponso m'mene analiri anthu, ndi m'menenso nkhondo inkayendera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Uriya atafika kwa Davide, Davide anamufunsa za momwe analili Yowabu, za asilikali ndi momwe nkhondo inkayendera. Onani mutuwo |