2 Samueli 11:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo m'mawa Davide analembera Yowabu kalata, wopita naye Uriya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo m'mawa Davide analembera Yowabu kalata, wopita naye Uriya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 M'maŵa mwake Davide adalembera Yowabu kalata, napatsira Uriya yemweyo kalatayo kuti akapereke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mmawa Davide analemba kalata kwa Yowabu ndipo anayitumiza ndi Uriya. Onani mutuwo |