2 Samueli 1:15 - Buku Lopatulika15 Davide naitana wina wa anyamatawo, nati, Sendera numkanthe. Ndipo anamkantha, nafa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Davide naitana wina wa anyamatawo, nati, Sendera numkanthe. Ndipo anamkantha, nafa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pomwepo Davide adaitana mmodzi mwa ankhondo ake, namuuza kuti, “Mtenge ameneyu, ukamuphe.” Wankhondoyo adamkanthadi naafa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kenaka Davide anayitana mmodzi mwa anyamata ake ndipo anati, “Pita ukamukanthe!” Kotero iye anapita kukamukantha, ndipo mnyamata uja anafa. Onani mutuwo |