2 Mafumu 4:3 - Buku Lopatulika3 Pamenepo anati, Kabwereke zotengera kwina kwa anansi ako onse, zotengera zopanda kanthu, zisakhale pang'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pamenepo anati, Kabwereke zotengera kwina kwa anansi ako onse, zotengera zopanda kanthu, zisakhale pang'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Apo Elisayo adamuuza kuti, “Pitani, kabwerekeni mitsuko yambirimbiri kwa anzanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Elisa anati, “Pita kabwereke mitsuko yonse yopanda kanthu kwa anzako. Usakabwereke mitsuko yochepa. Onani mutuwo |