2 Mafumu 10:2 - Buku Lopatulika2 Tsono ikakufikani inu kalata iyi, popeza muli nao ana a mbuye wanu, muli naonso magaleta ndi akavalo, ndi mizinda yalinga, ndi zida, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Tsono akakufikani inu kalata uyu, popeza muli nao ana a mbuye wanu, muli naonso magaleta ndi akavalo, ndi mudzi walinga, ndi zida, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Inu mukusamalira zidzukulu za mbuyanu Ahabu, ndipo muli nawo magaleta, zida zankhondo ndiponso mizinda yamalinga. Nchifukwa chake tsono mukangolandira kalatayi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Inu mukangolandira kalatayi, popeza ana a mbuye wanu ali ndi inu ndiponso muli ndi magaleta ndi akavalo, mzinda wotetezedwa ndi zida zankhondo, Onani mutuwo |