2 Akorinto 9:4 - Buku Lopatulika4 kuti kapena akandiperekeze a ku Masedoniya nadzakupezani inu osakonzeka, ife (kuti tisanene inu) tingachititsidwe manyazi m'kulimbika kumene. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 kuti kapena akandiperekeze a ku Masedoniya nadzakupezani inu osakonzeka, ife (kuti tisanene inu) tingachititsidwe manyazi m'kulimbika kumene. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ngati anthu ena a ku Masedoniya adzandiperekeze ndi kukupezani muli osakonzeka, tidzachita manyazi kwambiri kuti tinkakunyadirani pachabe, koma makamaka inuyo ndiye mudzachite manyazi kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pakuti nditabwera kumeneko ndi abale ena a ku Makedoniya, ndikukupezani kuti simunakonzeke, tingadzachite manyazi chifukwa chokudalirani. Koma amene angadzachite manyazi kwambiri ndi inuyo. Onani mutuwo |