2 Akorinto 9:14 - Buku Lopatulika14 ndipo iwo, ndi pempherero lao la kwa inu, akhumbitsa inu, chifukwa cha chisomo choposa cha Mulungu pa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndipo iwo, ndi pempherero lao la kwa inu, akhumbitsa inu, chifukwa cha chisomo choposa cha Mulungu pa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono adzakuwonetsani chikondi chao ndi kukupemphererani, chifukwa Mulungu wakukomerani mtima kopitirira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo iwowo adzakupemphererani mwachikondi chifukwa cha chisomo choposa chimene Ambuye wakupatsani. Onani mutuwo |