2 Akorinto 8:8 - Buku Lopatulika8 Sindinena ichi monga kulamulira, koma kuyesa mwa khama la ena choonadi cha chikondi chanunso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Sindinena ichi monga kulamulira, koma kuyesa mwa khama la ena choonadi cha chikondi chanunso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamene ndikunena zimenezi, sindikuchita kulamula ai. Pakukufotokozerani za changu cha ena, ndingofuna kuwona ngati chikondi chanu ndi chikondi chenicheni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Sindikukulamulirani, koma ndikufuna kuona ngati chikondi chanu nʼchoona pofananitsa ndi changu cha anthu ena. Onani mutuwo |