2 Akorinto 8:6 - Buku Lopatulika6 Kotero kuti tinadandaulira Tito, kuti monga anayamba kale, chomwechonso atsirize kwa inu chisomo ichinso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kotero kuti tinadandaulira Tito, kuti monga anayamba kale, chomwechonso atsirize kwa inu chisomo ichinso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nchifukwa chake tidaapempha Tito kuti akatsirizenso pakati panu ntchitoyi yakusonkhanitsa zopereka zachifundo imene iye anali atayamba kale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho tinamupempha Tito kuti atsirize poti nʼkuti atayamba kale ntchito yachisomoyi pakati panu. Onani mutuwo |