2 Akorinto 5:2 - Buku Lopatulika2 Pakutinso m'menemo tibuula, ndi kukhumbitsa kuvekedwa ndi chokhalamo chathu chochokera Kumwamba; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakutinso m'menemo tibuula, ndi kukhumbitsa kuvekedwa ndi chokhalamo chathu chochokera Kumwamba; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Nchifukwa chake tsono tikubuula ndi kulakalaka kuvala nyumba yathu yakumwambayo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pakali pano tibuwula, ndi kulakalaka kuvala nyumba yathu ya kumwambayo, Onani mutuwo |