2 Akorinto 4:17 - Buku Lopatulika17 Pakuti chisautso chathu chopepuka cha kanthawi chitichitira ife kulemera koposa kwakukulu ndi kosatha kwa ulemerero; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pakuti chisautso chathu chopepuka cha kanthawi chitichitira ife kulemera koposa kwakukulu ndi kosatha kwa ulemerero; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Masautso athu ndi opepuka, a nthaŵi yochepa, komabe akutitengera ulemerero umene uli waukulu kopambana, ndiponso wamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Pakuti masautso athu ndi opepuka ndi a kanthawi, koma akutitengera ulemerero wamuyaya umene ndi wopambana kwambiri. Onani mutuwo |