2 Akorinto 4:12 - Buku Lopatulika12 Chotero imfa ichita mwa ife, koma moyo mwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chotero imfa ichita mwa ife, koma moyo mwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Motero ife timaperekedwa ku imfa, koma chimenechi chimakupatsani moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Choncho imfa ikugwira ntchito mwa ife, koma moyo ukugwira ntchito mwa inu. Onani mutuwo |