2 Akorinto 4:10 - Buku Lopatulika10 nthawi zonse tilikusenzasenza m'thupi kufa kwake kwa Yesu, kuti moyonso wa Yesu uoneke m'thupi mwathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 nthawi zonse tilikusenzasenza m'thupi kufa kwake kwa Yesu, kuti moyonso wa Yesu uoneke m'thupi mwathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nthaŵi zonse tikuyenda nayo imfa ya Yesu m'thupi mwathu, kuti moyo wake uwonekenso m'thupi mwathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Nthawi zonse tikuyenda nayo imfa ya Yesu mʼthupi mwathu, kuti moyo wake Yesu uwonekenso mʼthupi mwathu. Onani mutuwo |