2 Akorinto 13:6 - Buku Lopatulika6 Koma ndiyembekeza kuti mudzazindikira kuti sitili osatsimikizidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma ndiyembekeza kuti mudzazindikira kuti sitili osatsimikizidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma ndikhulupirira kuti mudzazindikira kuti ife sitidalephere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo ndikhulupirira kuti mudzazindikira kuti ife sitinalephere mayesowo. Onani mutuwo |