2 Akorinto 11:21 - Buku Lopatulika21 Ndinena monga mwa kunyoza, monga ngati tinakhala ofooka. Koma m'mene wina alimbika mtimamo (ndinena mopanda nzeru) momwemo ndilimbika mtima inenso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndinena monga mwa kunyoza, monga ngati tinakhala ofooka. Koma m'mene wina alimbika mtimamo (ndinena mopanda nzeru) momwemo ndilimbika mtima inenso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ndikuvomera mwamanyazi kuti ife sitinali olimba mtima kuti nkuchita zotere. Tsopano ndilankhula ngati wopusa: zimene wina aliyense anganyadire, zomwezo inenso ndingathe kuzinyadira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndikuvomera mwamanyazi kuti ife sitinali olimba mtima kuti nʼkuchita zinthu zimenezi. Ndikuyankhula ngati chitsiru kuti chimene wina aliyense akhoza kudzitama nacho, Inenso ndikhoza kudzitama nachonso. Onani mutuwo |