2 Akorinto 1:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti monga masautso a Khristu atichulukira ife, choteronso chitonthozo chathu chichuluka mwa Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti monga masautso a Khristu atichulukira ife, choteronso chitonthozo chathu chichuluka mwa Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pakuti monga tikumva zoŵaŵa kwambiri pamodzi ndi Khristu, momwemonso Khristu amatilimbitsa mtima kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakuti monga momwe tili mʼmasautso pamodzi ndi Khristu, momwemonso Khristu amatitonthoza kwambiri. Onani mutuwo |