2 Akorinto 1:3 - Buku Lopatulika3 Wolemekezeka Mulungu ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate wa zifundo ndi Mulungu wa chitonthozo chonse, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Wolemekezeka Mulungu ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate wa zifundo ndi Mulungu wa chitonthozo chonse, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tiyamike Mulungu, Atate a Ambuye athu Yesu Khristu. Ndiwo Atate a chifundo ndi otilimbitsa mtima kwathunthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Alemekezeke Mulungu, Atate a Ambuye athu Yesu Khristu, Atate achifundo chonse, Mulungu wachitonthozo chonse. Onani mutuwo |