1 Samueli 7:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Aisraele anatuluka ku Mizipa, nathamangira Afilisti, nawakantha mpaka anafika pansi pa Betekara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Aisraele anatuluka ku Mizipa, nathamangira Afilisti, nawakantha mpaka anafika pansi pa Betekara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono Aisraele adatuluka ku Mizipa naŵalondola Afilistiwo, mpaka kubzola Betekara, akuŵapha njira yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Aisraeli anatuluka ku Mizipa kuthamangitsa Afilisti aja nʼkumawapha mʼnjira yonse mpaka kumunsi kwa Beti-Kari. Onani mutuwo |