1 Samueli 4:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo kunali, pakunena za likasa la Mulungu, iye anagwa chambuyo pa mpando wake pambali pa chipata, ndi khosi lake linathyoka, nafa iye; popeza anali wokalamba ndi wamkulu thupi. Ndipo adaweruza anthu a Israele zaka makumi anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo kunali, pakunena za likasa la Mulungu, iye anagwa chambuyo pa mpando wake pambali pa chipata, ndi khosi lake linathyoka, nafa iye; popeza anali wokalamba ndi wamkulu thupi. Ndipo adaweruza anthu a Israele zaka makumi anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamene adangotchula za Bokosi lachipangano la Chauta, Eli adagwa chankhongo, kuchoka pa mpando wake pafupi ndi chipata. Adathyoka khosi naafa, poti adaali wokalamba ndiponso wonenepa kwambiri. Anali atatsogolera Aisraele zaka makumi anai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Atangotchula Bokosi la Yehova, Eli anagwa chagada, kuchoka pa mpando wake umene unali mʼmbali mwa chitseko cha mpanda. Khosi lake linathyoka ndipo anafa, pakuti anali okalamba ndi onenepa kwambiri. Iye anatsogolera Israeli zaka makumi anayi. Onani mutuwo |