1 Samueli 30:9 - Buku Lopatulika9 Chomwecho Davide anamuka, iye ndi anthu mazana asanu ndi limodzi anali naye, nafika kukamtsinje Besori, pamenepo anatsala ena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chomwecho Davide anamuka, iye ndi anthu mazana asanu ndi limodzi anali naye, nafika kukamtsinje Besori, pamenepo anatsala ena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Choncho Davide adanyamuka pamodzi ndi anthu 600 amene anali naye. Ndipo adakafika ku mtsinje wa Besori nasiyako anthu ena. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Davide pamodzi ndi anthu ake 600 aja ananyamuka nafika ku mtsinje wa Besori. Kumeneko anasiyako anthu ena. Onani mutuwo |