1 Samueli 30:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Davide ananena ndi Abiyatara wansembeyo, mwana wa Ahimeleki, Unditengere kuno efodi. Abiyatara nabwera ndi efodi kwa Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Davide ananena ndi Abiyatara wansembeyo, mwana wa Ahimeleki, Unditengere kuno efodi. Abiyatara nabwera ndi efodi kwa Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamenepo Davide adauza wansembe Abiyatara, mwana wa Ahimeleki, kuti, “Undipatse efodi ija.” Abiyatara adampatsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka Davide anawuza wansembe Abiatara, mwana wa Ahimeleki kuti, “Ndipatse efodi ija.” Abiatara anabwera nayo efodiyo. Onani mutuwo |