Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 30:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo ena anapeza Mwejipito kuthengo, nabwera naye kwa Davide, nampatsa chakudya, nadya iye; nampatsanso madzi kumwa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo ena anapeza Mwejipito kuthengo, nabwera naye kwa Davide, nampatsa chakudya, nadya iye; nampatsanso madzi kumwa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Anthu amene anali ndi Davide, akuyenda m'njira, adapeza Mwejipito, nabwera naye kwa Davide. Tsono adampatsa buledi naadya. Adampatsanso madzi akumwa,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Anthu amene anali ndi Davide anapeza Mwigupto mʼmunda wina ndipo anabwera naye kwa Davide. Iwo anamupatsa madzi kuti amwe ndi chakudya kuti adye.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 30:11
9 Mawu Ofanana  

Mdani wako akamva njala umdyetse, akamva ludzu ummwetse madzi.


pakuti ndinali ndi njala, ndipo munandipatsa Ine kudya; ndinali ndi ludzu, ndipo munandimwetsa Ine; ndinali mlendo, ndipo munachereza Ine;


Musamanyansidwa naye Mwedomu, popeza ndiye mbale wanu; musamanyansidwa naye Mwejipito, popeza munali alendo m'dziko lake.


Ana obadwa nao a mbadwo wachitatu alowe m'msonkhano wa Yehova.


Ndipo Davide anawalondola, iye ndi anthu mazana anai; koma anthu mazana awiri anatsala m'mbuyo, chifukwa analema, osakhoza kuoloka kamtsinje Besori.


nampatsanso chigamphu cha nchinchi ya nkhuyu ndi nchinchi ziwiri za mphesa; ndipo atadya, moyo wake unabweranso mwa iye; pakuti adagona masiku atatu ndi usiku wao, osadya chakudya, osamwa madzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa