1 Samueli 28:20 - Buku Lopatulika20 Pomwepo Saulo anagwa pansi tantha, naopa kwakukulu, chifukwa cha mau a Samuele; ndipo analibe mphamvu; pakuti tsiku lonse ndi usiku wake wonse anakhala osadya kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pomwepo Saulo anagwa pansi tantha, naopa kwakukulu, chifukwa cha mau a Samuele; ndipo analibe mphamvu; pakuti tsiku lonse ndi usiku wake wonse anakhala osadya kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pompo Saulo adagwa pansi, kuchita kuti nyutu, ali wodzazidwa ndi mantha chifukwa cha mau a Samuele. Ndipo analibenso nyonga, poti sadadye kanthu tsiku lonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Nthawi yomweyo Sauli anagwa pansi atadzazidwa ndi mantha chifukwa cha mawu a Samueli. Analibenso mphamvu, pakuti sanadye tsiku lonse. Onani mutuwo |