1 Samueli 28:18 - Buku Lopatulika18 Chifukwa sunamvere mau a Yehova, ndi kukwaniritsa mkwiyo wake woopsa pa Amaleke, chifukwa chake Yehova wakuchitira chinthu ichi lero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Chifukwa sunamvera mau a Yehova, ndi kukwaniritsa mkwiyo wake woopsa pa Amaleke, chifukwa chake Yehova wakuchitira chinthu ichi lero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Chauta akuchita zimenezi lero, chifukwa chakuti sudamvere mau ake, ndipo sudaonongeretu Aamaleke ndi zinthu zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yehova wachita zimenezi lero chifukwa sunamvere mawu ake ndipo sunawawonongeretu Aamaleki. Onani mutuwo |