1 Samueli 28:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mkaziyo pakuona Samuele, anafuula ndi mau aakulu; ndi mkaziyo analankhula ndi Saulo, nati, Munandinyengeranji? Popeza inu ndinu Saulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo mkaziyo pakuona Samuele, anafuula ndi mau akulu; ndi mkaziyo analankhula ndi Saulo, nati, Munandinyengeranji? Popeza inu ndinu Saulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamene mkaziyo adaona Samuele, adakuwa kwambiri nati, “Chifukwa chiyani mwandinyenga? Ndinu mfumu Saulo!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamene mkaziyo anaona Samueli anakuwa kwambiri, nawuza Sauli kuti, “Nʼchifukwa chiyani inu mwandipusitsa? Inu ndinu Sauli!” Onani mutuwo |