1 Samueli 28:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Saulo anamlumbirira kwa Yehova, nati, Pali Yehova, palibe chilango chidzakugwera chifukwa cha chinthu ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Saulo anamlumbirira kwa Yehova, nati, Pali Yehova, palibe chilango chidzakugwera chifukwa cha chinthu ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Koma Saulo adalonjeza mkaziyo molumbira nati, “Pali Chauta wamoyo, sudzalangidwa kaamba ka zimenezi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Koma Sauli analonjeza mkaziyo molumbira nati, “Pali Yehova wamoyo, iweyo sudzalangidwa chifukwa cha zimenezi.” Onani mutuwo |