1 Samueli 25:16 - Buku Lopatulika16 iwo anatikhalira ngati linga usana ndi usiku, nthawi yonse tinali nao ndi kusunga nkhosazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 iwo anatikhalira ngati linga usana ndi usiku, nthawi yonse tinali nao ndi kusunga nkhosazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ankatichinjiriza ngati linga usana ndi usiku, nthaŵi zonse pamene tinali ndi iwowo poŵeta nkhosa ku Rama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ankatitchinjiriza ngati mpanda usiku ndi usana nthawi yonse tinkaweta nkhosa. Onani mutuwo |