Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 21:3 - Buku Lopatulika

3 Chifukwa chake tsono muli ndi chiyani? Mundipatse m'dzanja langa mikate isanu, kapena chilichonse muli nacho.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Chifukwa chake tsono muli ndi chiyani? Mundipatse m'dzanja langa mikate isanu, kapena chilichonse muli nacho.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kodi muli ndi chakudya? Mundipatseko mitanda isanu yabuledi kapena chakudya chilichonse chimene muli nacho pano.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kodi muli ndi chakudya? Patseniko malofu a buledi asanu, kapena chilichonse muli nacho.”

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 21:3
4 Mawu Ofanana  

Pamene mwamuna adzamgwira mbale wake m'nyumba ya atate wake, nadzati, Iwe uli ndi chovala, khala wolamulira wathu, ndi kupasula kumeneku kukhale m'dzanja lako;


Mwenzi anthu awa akadakhala m'dzanja langa; ndikadamchotsadi Abimeleki. Ndipo anati kwa Abimeleki, Chulukitsa khamu lako, nutuluke.


Nati Davide kwa Ahimeleki wansembeyo, Mfumu inandilamulira ntchito, ninena nane, Asadziwe munthu aliyense kanthu za ntchito imene ndakutumira ndi kukulamulira; ndipo ndawapanga anyamatawo ku malo akuti.


Ndipo wansembeyo anayankha Davide nati, Ndilibe mkate wachabe, koma ulipo mkate wopatulika; pokhapo ngati anyamatawo anadzisunga kupewa akazi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa