1 Samueli 2:31 - Buku Lopatulika31 Ona, masiku alinkudza amene ndidzadula dzanja lako, ndi dzanja la nyumba ya kholo lako, kuti m'banja lako musakhalenso nkhalamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ona, masiku alinkudza amene ndidzadula dzanja lako, ndi dzanja la nyumba ya kholo lako, kuti m'banja lako musakhalenso nkhalamba, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndithudi, masiku akudza pamene ndidzachotse anyamata onse a m'banja la atate ako, kotero kuti siidzapezekanso nkhalamba pabanja pako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Nthawi ikubwera imene ndidzachotsa anyamata ako ndi anyamata a pa banja la abambo ako, kotero kuti sipadzakhala munthu wokalamba pa banja lako. Onani mutuwo |