1 Samueli 2:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo mwanayo Samuele anakulakula, ndipo Yehova ndi anthu omwe anamkomera mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo mwanayo Samuele anakulakula, ndipo Yehova ndi anthu omwe anamkomera mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Monsemo mnyamata uja Samuele ankakulabe mu msinkhu, ndipo ankapeza kuyanja pamaso pa Chauta ndi anthu omwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ndipo mnyamata Samueli anapitirira kukula mu msinkhu, ndipo ankapeza kuyanja pamaso pa Yehova ndi anthu. Onani mutuwo |