1 Samueli 19:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yonatani analankhula ndi Saulo atate wake movomereza Davide, nanena naye, Mfumu asachimwire mnyamata wake Davide; chifukwa iyeyo sanachimwire inu, ndipo ntchito zake anakuchitirani zinali zabwino ndithu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yonatani analankhula ndi Saulo atate wake movomereza Davide, nanena naye, Mfumu asachimwire mnyamata wake Davide; chifukwa iyeyo sanachimwire inu, ndipo ntchito zake anakuchitirani zinali zabwino ndithu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono Yonatani adaterodi ndipo adakanena zabwino za Davide kwa bambo wake, namuuza kuti, “Atate, musachimwire mtumiki wanu Davide, poti sadakuchimwireni, koma amakuchitirani zabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tsono Yonatani anakanena zabwino za Davide kwa abambo ake Sauli ndipo anati, “Mfumu musachimwire mtumiki wanu Davide, sanakuchimwireni, koma amakuchitirani zabwino kwambiri. Onani mutuwo |