1 Samueli 18:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Mikala mwana wamkazi wa Saulo anakonda Davide; ndipo pakumva Saulo, anakondwera nako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Mikala mwana wamkazi wa Saulo anakonda Davide; ndipo pakumva Saulo, anakondwera nako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Komabe Mikala, mwana wina wamkazi wa Saulo, ankakonda Davide. Saulo atamva, adakondwa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma Mikala mwana wamkazi wa Sauli anamukonda Davide ndipo Sauli atamva za zimenezi, anakondwera. Onani mutuwo |