1 Samueli 17:19 - Buku Lopatulika19 Tsono Saulo, ndi iwowa, ndi anthu onse a Israele, anali m'chigwa cha Ela, ku nkhondo ya Afilisti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Tsono Saulo, ndi iwowa, ndi anthu onse a Israele, anali m'chigwa cha Ela, ku nkhondo ya Afilisti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Saulo, abale akowo ndi Aisraele ena, akumenyana nkhondo ndi Afilisti ku chigwa cha Ela.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Sauli, abale akowo ndi asilikali onse a Israeli ali ku chigwa cha Ela, akumenyana ndi Afilisti.” Onani mutuwo |