1 Samueli 15:25 - Buku Lopatulika25 Chifukwa chake tsono, mukhululukire tchimo langa, nimubwerere pamodzi ndi ine, kuti ndikalambire Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Chifukwa chake tsono, mukhululukire tchimo langa, nimubwerere pamodzi ndi ine, kuti ndikalambire Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Nchifukwa chake tsono pepani, ndagwira mwendo, mundikhululukire tchimo langa, ndipo mubwerere nane pamodzi, kuti ndikampembedze Chauta.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Tsopano ndikukupemphani, khululukireni tchimo langa ndipo mubwerere nane kuti ndikapembedze Yehova.” Onani mutuwo |