Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 14:5 - Buku Lopatulika

5 Phiri lija linaimirira kuyang'ana kumpoto pandunji pa Mikimasi, ndi linzake kumwera pandunji pa Geba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Phiri lija linaimirira kuyang'ana kumpoto pandunji pa Mikimasi, ndi linzake kumwera pandunji pa Geba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Thanthwe lina linali kumpoto kuyang'anana ndi Mikimasi, ndipo linalo linali kumwera kuyang'anana ndi Geba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Thanthwe limodzi linali chakumpoto kuyangʼanana ndi Mikimasi, ndipo thanthwe linalo linali chakummwera kuyangʼanana ndi Geba.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 14:5
10 Mawu Ofanana  

ndi Ibara, ndi Elisama, ndi Elifeleti,


Wafika ku Ayati, wapitirira kunka ku Migironi; pa Mikimasi asunga akatundu ake;


wapita pampata; wagona pa Geba, Rama anthunthumira; Gibea wa Saulo wathawa.


Ndipo Samuele anati, Mwachitanji? Nati Saulo, Chifukwa ndinaona kuti anthuwo alinkubalalika kundisiya ine, ndi kuti inu simunafike masiku aja tinapangana, ndi kuti Afilisti anasonkhana ku Mikimasi;


Pamenepo Saulo anadzisankhira anthu zikwi zitatu a Israele; zikwi za iwowa zinali ndi Saulo ku Mikimasi, ndi kuphiri la ku Betele; ndi chikwi chimodzi anali ndi Yonatani ku Gibea wa ku Benjamini; ndipo anawauza anthu ena onse amuke ku mahema ao.


Ndipo a ku kaboma ka Afilisti anatuluka kunja ku mpata wa ku Mikimasi.


Ndipo Yonatani anathyola kaboma ka Afilisti lokhala ku Geba, ndipo Afilisti anamva za ichi. Ndipo Saulo analiza lipenga m'dziko monse, nati, Amve Ahebri.


Ndipo anakantha Afilisti tsiku lija kuyambira ku Mikimasi kufikira ku Ayaloni, ndipo anthu anafooka kwambiri.


Ndipo pakati pa mipata imene Yonatani anafuna kupitapo kunka ku kaboma ka Afilisti, panali phiri lathanthwe pa mbali ina, ndi phiri lathanthwe pa mbali inzake; ndipo dzina la linalo ndilo Bozezi, ndi la linzake ndilo Sene.


Ndipo Yonatani ananena ndi mnyamata wonyamula zida zake, Tiye tipite ku kaboma ka osadulidwa awa; kapena Yehova adzatigwirira ntchito; pakuti palibe chomletsa Yehova kupulumutsa angakhale ndi ambiri kapena ndi owerengeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa