1 Samueli 14:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Saulo analikukhala m'matsekerezo a Gibea patsinde pa mtengo wankhangaza uli ku Migironi; ndipo panali naye anthu monga mazana asanu ndi limodzi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Saulo analikukhala m'matsekerezo a Gibea patsinde pa mtengo wankhangaza uli ku Migironi; ndipo panali naye anthu monga mazana asanu ndi limodzi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Saulo ankakhala m'malire a Gibea patsinde pa mtengo wa makangaza ku Migironi. Anthu amene anali naye analipo 600 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Sauli ankakhala mʼmalire a Gibeya pa tsinde pa mtengo wamakangadza ku Migironi. Anthu amene anali naye analipo 600. Onani mutuwo |