Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 12:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo Samuele anauza Aisraele onse, kuti, Onani ndinamvera mau anu mwa zonse munalankhula ndi ine, ndipo ndinakulongerani mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo Samuele anauza Aisraele onse, kuti, Onani ndinamvera mau anu mwa zonse munalankhula ndi ine, ndipo ndinakulongerani mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Pambuyo pake Samuele adauza Aisraele onse kuti, “Ndidamvera zonse zimene mudandiwuza, ndipo ndakupatsani mfumu kuti izikulamulirani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Pambuyo pake Samueli anawuza Aisraeli onse kuti, “Ine ndamvera zonse zimene munandiwuza ndipo ndakupatsani mfumu kuti izikulamulirani.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 12:1
7 Mawu Ofanana  

Ndinakupatsa mfumu mu mkwiyo wanga; ndinamchotsanso mu ukali wanga.


Pamenepo Samuele anatenga nsupa ya mafuta, nawatsanulira pamutu pake, nampsompsona iye, nati, Sanakudzozeni ndi Yehova kodi, Mukhale mfumu ya pa cholowa chake?


Ndipo Samuele ananena ndi anthu onse, Mumuona kodi iye amene Yehova anamsankha, kuti palibe wina wakufanana naye pakati pa anthu onse? Ndipo anthu onse anafuula, kuti, Akhale ndi moyo mfumuyo.


Chifukwa chake tsono umvere mau ao; koma uwachenjeze kolimba, ndi kuwadziwitsa makhalidwe ake a mfumu imene idzawaweruza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa