1 Samueli 11:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo mzimu wa Mulungu unamgwera Saulo mwamphamvu, pamene anamva mau awa, ndi mkwiyo wake unayaka kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo mzimu wa Mulungu unamgwera Saulo mwamphamvu, pamene anamva mau awa, ndi mkwiyo wake unayaka kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Saulo atamva zimenezi, pomwepo mzimu wa Mulungu udamloŵa mwamphamvu, ndipo adapsa mtima kwabasi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Sauli atamva mawu awo, Mzimu wa Mulungu unabwera pa iye mwa mphamvu ndipo anakwiya kwambiri. Onani mutuwo |