1 Samueli 10:26 - Buku Lopatulika26 Ndi Saulo yemwe anamuka kunyumba yake ku Gibea; ndipo am'khamu anatsagana naye iwo amene Mulungu adakhudza mitima yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndi Saulo yemwe anamuka kunyumba yake ku Gibea; ndipo am'khamu anatsagana naye iwo amene Mulungu adakhudza mitima yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Saulo nayenso adapita kwao ku Gibea, ndipo adatsakana naye anthu amphamvu amene Mulungu adaŵafeŵetsa mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Sauli anapitanso ku mudzi kwawo ku Gibeya, pamodzi ndi anthu amphamvu amene Mulungu anawafewetsa mitima. Onani mutuwo |