1 Samueli 10:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pamene anafika ku Gibea, onani, gulu la aneneri linakomana naye; ndi Mzimu wa Mulungu unamgwera mwamphamvu, iye nanenera pakati pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pamene anafika ku Gibea, onani, gulu la aneneri linakomana naye; ndi Mzimu wa Mulungu unamgwera mwamphamvu, iye nanenera pakati pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Atafika ku Gibea, adakumana ndi gulu la aneneri. Tsono mzimu wa Mulungu udamloŵa Sauloyo mwamphamvu, nayamba kulosa nao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Atafika ku Gibeya, anakumana ndi gulu la aneneri. Mzimu wa Mulungu unabwera pa iye mwamphamvu, nayamba kulosa nawo. Onani mutuwo |