1 Samueli 1:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo munthuyo Elikana, ndi a pa banja lake onse, anakwera kukapereka kwa Yehova nsembe ya chaka ndi chaka, ndi ya chowinda chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo munthuyo Elikana, ndi a pa banja lake onse, anakwera kukapereka kwa Yehova nsembe ya chaka ndi chaka, ndi ya chowinda chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono Elikana ndi banja lake lonse adapitanso kukatsira nsembe ya chaka ndi chaka kwa Chauta, ndi kukakwaniritsa lonjezo lake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Elikana ndi banja lake lonse anapita kukapereka nsembe ya pa chaka kwa Yehova ndi kukakwaniritsa malonjezo ake. Onani mutuwo |