1 Akorinto 9:6 - Buku Lopatulika6 Kapena kodi ife tokha, Barnabasi ndi ine tilibe ulamuliro wakusagwira ntchito? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kapena kodi ife tokha, Barnabasi ndi ine tilibe ulamuliro wakusagwira ntchito? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kodi ine ndi Barnabasi, ndife tokha oyenera kugwira ntchito zamanja kuti tizidzipezera tokha zotisoŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kodi kapena ine ndekha ndi Barnaba ndiye tikuyenera kugwira ntchito kuti tipeze zotisowa? Onani mutuwo |